Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

March 21-27

YOBU 6-10

March 21-27
 • Nyimbo Na. 68 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yobu Anasonyeza Kukhumudwa Kwake”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yobu 6:14—Kodi Yobu anasonyeza bwanji kuti kukoma mtima kosatha n’kofunika? (w10 11/15 32 ndime 20)

  • Yobu 7:9, 10; 10:21—Ngati Yobu ankakhulupirira kuti akufa adzauka, n’chifukwa chiyani ananena zimene zili m’mavesiwa? (w06 3/15 14 ndime 11)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: Yobu 9:1-21 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: wp16.2 16—Muuzeni munthu amene mukumulalikirayo kuti angathe kupereka ndalama zothandizira ntchito yathu yapadziko lonse. (Osapitirira 2 min.)

 • Ulendo Wobwereza: wp16.2 16—Muuzeni nkhani imene mudzaphunzire ulendo wotsatira. (Osapitirira 4 min.)

 • Phunziro la Baibulo: fg phunziro 2 ndime 6-8 (Osapitirira 6 min.)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 114

 • Muzichita Zinthu Mozindikira Mukamalimbikitsa Ena: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo imene akulu anaonera pa Sukulu ya Utumiki wa Ufumu yomwe inachitika posachedwapa. Kenako pemphani omvera kuti afotokoze mmene abale awiri a m’vidiyoyi asonyezera chitsanzo chabwino polimbikitsa munthu amene wakhumudwa chifukwa cha imfa ya munthu amene amam’konda.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 27 ndime 19-22 ndi bokosi patsamba 279 (30 min.)

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 27 ndi Pemphero