Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  March 2016

March 14-20

YOBU 1-5

March 14-20
 • Nyimbo Na. 89 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yobu Anakhalabe Wokhulupirika Pamene Ankayesedwa”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yobu 1:6; 2:1—Kodi ndi ndani amene ankaloledwa kukaonekera kwa Yehova? (w06 3/15 13 ndime 6)

  • Yobu 4:7, 18, 19—Kodi ndi zinthu zabodza ziti zimene Elifazi anauza Yobu? (w14 3/15 13 ndime 3; w05 9/15 26 ndime 4-5; w95 2/15 27 ndime 5-6)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: Yobu 4:1-21 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 88

 • Musamangotengera Zochita za Anzanu: (15 min.) Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuonetsa vidiyo ya pa jw.org yakuti Musamangotengera Zochita za Anzanu (Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA.) Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi ana amakumana ndi mavuto otani kusukulu? Kodi angagwiritse ntchito bwanji mfundo ya pa Ekisodo 23:2? Kodi ndi zinthu 4 ziti zimene zingawathandize kuti asamangotengera zochita za anzawo komanso kuti akhalebe okhulupirika kwa Mulungu? Pemphani achinyamata kuti afotokoze zinthu zabwino zimene anakumana nazo kusukulu.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 27 ndime 10-18 (30 min.)

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 149 ndi Pemphero