6:11-17

Mtumwi Paulo anayerekezera Akhristu ndi asilikali omwe akumenya nkhondo. Adani athu ndi “makamu a mizimu yoipa.” Ngakhale timaoneka ofooka komanso osatetezeka, tingapambane nkhondoyi ngati titavala “zida zonse zankhondo zochokera kwa Mulungu.”

Tchulani dzina la chida chilichonse komanso zimene chikutanthauza

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi ndimavala zida zonse zankhondo?