1:8-10

Ulamuliro wa Yehova ukugwirizanitsa anthu komanso angelo.

  • Ukukonzekeretsa Akhristu odzozedwa kuti akalamulire kumwamba motsogoleredwa ndi Yesu Khristu

  • Ukukonzekeretsa anthu omwe adzakhale padziko lapansi n’kumalamuliridwa ndi Ufumu wa Mesiya

Kodi ndi zinthu ziti zomwe ndingachite pothandiza kuti tizikhala ogwirizana m’gulu la Yehova?