Satana amafuna kuwononga ubwenzi wathu ndi Yehova pogwiritsa ntchito zimene mtima wathu umalakalaka. Iye amayesa munthu aliyense mogwirizana ndi zimene amalakalaka komanso zomwe zikuchitika pa moyo wake.

Kodi Yesu anagwiritsa ntchito chiyani pokana mayesero atatu amene Satana amagwiritsa ntchito kwambiri? (Aheb. 4:12; 1 Yoh. 2:15, 16) Nanga kodi ndingamutsanzire bwanji?

  • 4:1-4

    “Chilakolako cha thupi”

  • 4:5-8

    “Chilakolako cha maso”

  • 4:9-12

    “Kudzionetsera”