• Nyimbo Na. 75 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Ezekieli Ankasangalala Kulengeza Uthenga wa Mulungu”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Ezek. 1:20, 21, 26-28​—Kodi galeta lakumwamba limaimira chiyani? (w07 7/1 11 ¶6)

  • Ezek. 4:1-7​—Kodi Ezekieli anachitadi zinthu zofanizira kuzingidwa kwa Yerusalemu? (w07 7/1 12 ¶4)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 1:1-14

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU