Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  June 2017

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MALIRO 1-5

Mtima Wodikira Umatithandiza Kuti Tipirire

Mtima Wodikira Umatithandiza Kuti Tipirire

Kodi n’chiyani chinathandiza kuti Yeremiya apirire ngakhale kuti anakumana ndi mavuto aakulu?

3:20, 21, 24, 26, 27

  • Iye ankakhulupirira ndi mtima wonse kuti Yehova ‘adzaweramira’ anthu ake omwe analapa n’kuwapulumutsa m’mavuto awo

  • Iye anaphunzira ‘kunyamula goli lake ali mnyamata.’ Munthu akamapirira mayesero ali wamng’ono zimamuthandiza kuti adzathe kupirira mavuto omwe angadzakumane nawo m’tsogolo

Kodi ndingakonzekere bwanji mavuto amene ndingakumane nawo m’tsogolo?

 

Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndili ndi mtima wodikira?