• Nyimbo Na. 128 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Mtima Wodikira Umatithandiza Kuti Tipirire”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Maliro 2:17​—Kodi ndi mawu ati kwenikweni amene Yehova “ananena” okhudza Yerusalemu? (w07 6/1 9 ¶2)

  • Maliro 5:7​—Kodi Yehova amaimba anthu mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo awo akale? (w07 6/1 10 ¶5)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliro 2:20–3:12

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.3 chikuto​—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.3 chikuto​—Muitanireni kumisonkhano yathu.

 • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w11 9/15 9-10 ¶11-13​—Mutu: Yehova Ndi Cholowa Changa.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 126

 • Zofunika Pampingo: (8 min.) Mukhoza kukambirana “Kalata Yochokera ku Bungwe Lolamulira” ya mu Buku Lapachaka. (yb 17 2-5)

 • Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lathu Lachita ya June 2017.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 2 ¶13-22

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 100 ndi Pemphero