Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  June 2017

June 5-11

YEREMIYA 51-52

June 5-11
 • Nyimbo Na. 37 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Nthawi Zonse Mawu a Yehova Amakwaniritsidwa”: (10 min.)

  • Yer. 51:11, 28​—Yehova ananeneratu za munthu amene adzagonjetse Babulo (it-2-E 360 ¶2-3)

  • Yer. 51:30​—Yehova ananeneratu kuti Babulo adzawonongedwa (it-2-E 459 ¶4)

  • Yer. 51:37, 62​—Yehova ananeneratu kuti Babulo adzakhala bwinja (it-1-E 237 ¶1)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yer. 51:25​—Kodi n’chifukwa chiyani Babulo akutchulidwa kuti ndi “phiri lowononga”? (it-2-E 444 ¶9)

  • Yer. 51:42​—Kodi “nyanja” imene ‘idzasefukire ndi kumiza Babulo,’ ikuimira chiyani? (it-2-E 882 ¶3)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 51:1-11

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Kukambirana “Zitsanzo za Ulaliki.” Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo. Limbikitsani ofalitsa kuti azionetsa mwininyumba zimene zili pa webusaiti yathu ya jw.org/ny pa gawo lakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU