GALAMUKANI!

Perekani Magaziniyo: Galamukani! iyi ikufotokoza nkhani yochititsa chidwi. [Mpatseni magaziniyo.]

Funso: Kodi mukudziwa kuti a Mboni za Yehova amamasulira mabuku m’zinenero zoposa 750?

Lemba: Chiv. 14:6

GALAMUKANI!

Funso: Kodi mukuona kuti mfundo iyi ingathandize anthu okwatirana pamene akukambirana vuto linalake?

Lemba: Yak. 1:19

Perekani magaziniyo: [Musonyezeni nkhani yomwe yayambira patsamba 10.] Nkhaniyi ikufotokoza mfundo zinanso za m’Baibulo zomwe zingathandize anthu okwatirana.

TIMAPEPALA

Funso: Taonani funso ili. [Werengani funso lomwe lili pakapepalako losonyeza mayankho angapo.] Inuyo mukuganiza bwanji?

Lemba: [Lili patsamba 2 la kapepalako]

Perekani Kapepalako: Kapepalaka kakufotokoza zimene mungaphunzire palembali.

LEMBANI NJIRA INA IMENE MUNGAGWIRITSE NTCHITO

Potengera zitsanzozi, konzani njira imene mungagwiritse ntchito.