Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  June 2016

June 6-12

MASALIMO 34-37

June 6-12
 • Nyimbo Na. 95 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Khulupirira Yehova Ndipo Chita Zabwino”: (10 min.)

  • Sal. 37:1, 2—Pitirizani kutumikira Yehova osati kusirira anthu ochita zosalungama omwe akuoneka ngati zinthu zikuwayendera bwino (w03 12/1 9-10 ndime 3-6)

  • Sal. 37:3-6—Muzikhulupilira Yehova, muzichita zabwino ndipo iye adzakudalitsani (w03 12/1 10-12 ndime 7-15)

  • Sal. 37:7-11—Muziyembekezera Yehova moleza mtima kuti adzachotse anthu oipa (w03 12/1 13 ndime 16-20)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Sal. 34:18—Kodi Yehova amayankha bwanji mapemphero a “anthu a mtima wosweka” ndiponso “odzimvera chisoni mumtima mwawo”? (w11 6/1 19)

  • Sal. 34:20—Kodi ulosiwu unakwaniritsidwa bwanji pa Yesu? (w13 12/15 21 ndime 19)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 35:19–36:12

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse payokha, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo. Limbikitsani ofalitsa kuti alembe ulaliki wawowawo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU