Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 38-44

Yehova Amasamalira Anthu Omwe Akudwala

Yehova Amasamalira Anthu Omwe Akudwala

Anthu amene amatumikira Yehova mokhulupirika amamudalira pa mavuto aliwonse

41:1-4

  • Davide anadwala kwambiri

  • Davide ankathandiza anthu onyozeka

  • Davide sankayembekezera kuti achira mozizwitsa, koma anapempha Yehova kuti amupatse nzeru, amutonthoze ndiponso amuthandize

  • Yehova ankaona kuti Davide anali munthu wokhulupirika