Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  June 2016

 MOYO WATHU WACHIKHRISTU

“Mulungu Ndiye Mthandizi Wanga”

“Mulungu Ndiye Mthandizi Wanga”

Masalimo 52–59 amasonyeza mmene Davide ankamvera pa nthawi yomwe ankakumana ndi mavuto. Komabe anakhulupirira Yehova pa nthawi yovutayi. (Sal. 54:4; 55:22) Iye anatamandanso Yehova chifukwa cha Mawu ake. (Sal. 56:10) Kodi ifeyo timakhulupirira komanso kudalira Mulungu ngati mmene Davide ankachitira? Kodi tikakumana ndi mavuto, timafufuza malangizo m’Mawu a Yehova? (Miy. 2:6) Kodi ndi mavesi ati omwe anakuthandizani pamene . . .

  • munafooka kapena kuvutika maganizo?

  • munkadwala?

  • ena anakukhumudwitsani?

  • munkazunzidwa?