Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 TIMOTEYO 4-6

Kukhala Wodzipereka kwa Mulungu N’kofunika Kuposa Chuma

Kukhala Wodzipereka kwa Mulungu N’kofunika Kuposa Chuma

6:6-10

Kodi malemba otsatirawa akusonyeza bwanji kuti tingakhale osangalala kwambiri ngati titakhala wodzipereka kwa Mulungu m’malo mofunafuna chuma?

N’chifukwa chiyani n’zosatheka kukhala wodzipereka kwa Mulungu pa nthawi imodzimodziyo n’kumafunafuna chuma? (Mat. 6:24)