Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 TIMOTEYO 1-3

Yesetsani Kuti Mukhale Oyang’anira

Yesetsani Kuti Mukhale Oyang’anira

3:1, 13

Zimakhala bwino kwambiri abale akayamba kuchita zambiri mumpingo adakali aang’ono. Zimenezi zimawapatsa mpata woti asonyeze kuti ndi woyenerera kudzakhala atumiki othandiza akadzakula. (1 Tim. 3:10) Kodi m’bale angatani kuti akhale ndi udindo mumpingo? Ayenera kuyesetsa kumachita zinthu zotsatirazi:

  • Kudzipereka.​—km 7/13 2-3 ¶2

  • Kukonda zinthu zauzimu.​—km 7/13 3 ¶3

  • Kukhala wodalirika komanso wokhulupirika.—km 7/13 3 ¶4