Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

July 22-​28

1 TIMOTEYO 1-3

July 22-​28

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yesetsani Kuti Mukhale Oyang’anira”: (10 min.)

  • [Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 1 Timoteyo.]

  • 1 Tim. 3:1​—Abale onse akulimbikitsidwa kuti aziyesetsa kuti akhale oyang’anira mumpingo (w16.08 21 ¶3)

  • 1 Tim. 3:13​—Abale amene amatumikira bwino amalandira madalitso ambiri (km 9/78 4 ¶7)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • 1 Tim. 1:4​—N’chifukwa chiyani Paulo anachenjeza Timoteyo kuti asamataye nthawi kukambirana ndi anthu nkhani zokhudza mibadwo ya makolo? (it-1 914-915)

  • 1 Tim. 1:17​—N’chifukwa chiyani Yehova yekha ndi amene ayenera kutchedwa “Mfumu yamuyaya”? (cl 12 ¶15)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 1 Tim. 2:1-15 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU