●○○ ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi anthu okwatirana angatani kuti banja lawo likhale lolimba?

Lemba: Aef. 5:33

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi makolo angatani kuti ana awo akule bwino?

○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA

Funso: Kodi makolo angatani kuti ana awo akule bwino?

Lemba: Miy. 22:6

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi ana angatani kuti zinthu ziziwayendera bwino?

○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI

Funso: Kodi ana angatani kuti zinthu ziziwayendera bwino?

Lemba: Miy. 4:5, 6

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi ndi kuti kumene tingapeze malangizo amene angatithandize pa moyo wathu?