CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Fanizo la Mwana Wolowerera”: (10 min.)

  • Luka 15:11-16​—Mwana wolowerera anawononga cholowa chake pochita makhalidwe oipa (nwtsty mfundo zimene ndikuphunzira)

  • Luka 15:17-24​—Iye anadzimvera chisoni ndipo bambo ake anamuchitira chifundo n’kumulandiranso (nwtsty mfundo zimene ndikuphunzira)

  • Luka 15:25-32​—Bambo anathandiza mwana wake wamkulu kuti ayambe kuona zinthu moyenera

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Luka 14:26​—Kodi mawu akuti ‘kudana’ pavesili akutanthauza chiyani? (nwtsty mfundo zimene ndikuphunzira)

  • Luka 16:10-13​—Kodi Yesu ankatanthauza chiyani pamene ananena za “chuma chosalungama”? (w17.07 8-9 ¶7-8)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 14:1-14

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha zimene tinganene. Kenako muitanireni kumisonkhano yathu.

 • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse ndipo gawirani buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 32 ¶14-15

MOYO WATHU WACHIKHRISTU