CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Muzikhala Owolowa Manja”: (10 min.)

  • Luka 6:37​—Ngati tikufuna kuti anthu ena azitikhululukira, ifenso tizikhululuka (“Pitirizani kukhululukira anthu machimo awo ndipo machimo anunso adzakhululukidwa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 6:37, nwtsty; w08 5/15 9-10 ¶13-14)

  • Luka 6:38​—Tizikhala ndi chizolowezi chogawira ena zinthu (“Khalani opatsa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 6:38, nwtsty)

  • Luka 6:38​—Muyezo umene tikuyezera ena, iwonso adzatiyezera womwewo (“m’matumba anu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 6:38, nwtsty)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Luka 6:12, 13​—Kodi Akhristu amene akufuna kupanga zosankha zikuluzikulu angatsanzire bwanji Yesu? (w07 8/1 6 ¶1)

  • Luka 7:35​—Kodi mawu a Yesu palembali angatithandize bwanji ngati ena akutinenera zoipa? (“zotsatira zake” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 7:35, nwtsty)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 7:36-50

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 108

 • Muzitsanzira Yehova Pokhala Owolowa Manja: (15 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa:

  • Kodi Yehova ndi Yesu amasonyeza bwanji kuti ndi owolowa manja?

  • Kodi Yehova amatidalitsa bwanji tikakhala owolowa manja?

  • Kodi tingasonyeze bwanji kuti ndife owolowa manja pa nkhani yokhululukira ena?

  • Kodi tingasonyeze bwanji kuti ndife owolowa manja pa nkhani ya mmene timagwiritsira ntchito nthawi yathu?

  • Kodi tingasonyeze bwanji kuwolowa manja pa nkhani yoyamikira ena?

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 21 ¶1-7 komanso tsamba 220-221

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 57 ndi Pemphero