Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  July 2017

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 15-17

Kodi Mumakwaniritsa Zimene Mwalonjeza?

Kodi Mumakwaniritsa Zimene Mwalonjeza?

17:18, 19

  • Kodi Mfumu Zedekiya inaswa pangano lotani?

    Kodi inakumana ndi zotani chifukwa cha kuswa panganoli?

  • Kodi ineyo ndinapanga malonjezo otani?

    Kodi ndi zinthu ziti zimene zingachitike ngati nditaswa malonjezowa?