Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  July 2017

July 10-16

EZEKIELI 15-17

July 10-16
 • Nyimbo Na. 11 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Kodi Mumakwaniritsa Zimene Mwalonjeza?”: (10 min.)

  • Ezek. 17:1-4​—Ababulo anachotsa Mfumu Yehoyakini pampando n’kuikapo Zedekiya (w07 7/1 12 ¶6)

  • Ezek. 17:7, 15​—Zedekiya sanakhulupirike, m’malomwake anapempha thandizo kwa Aiguputo (w07 7/1 12 ¶6)

  • Ezek. 17:18, 19​—Yehova ankafuna kuti Zedekiya akwaniritse zomwe analonjeza (w12 10/15 30 ¶11; w88 9/15 17 ¶8)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Ezek. 16:60​—Kodi “pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale,” ndi chiyani, ndipo ndi ndani ali m’panganoli? (w88 9/15 17 ¶7)

  • Ezek. 17:22, 23​—Kodi ndi ndani amene ali “nsonga yanthete” yomwe Yehova anati adzabzala? (w07 7/1 12 ¶6)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 16:28-42

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU