Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  July 2017

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 18-20

Kodi Yehova Akatikhululukira Machimo, Amawakumbukirabe?

18:21, 22

  • Yehova akatikhululukira machimo, sangadzatiimbenso mlandu pa zolakwazo m’tsogolo.

Zitsanzo za m’Baibulo zotsatirazi zimatithandiza kukhulupirira kuti Yehova amakhululuka.

Mfumu Davide

  • Kodi ndi zoipa zotani zimene anachita?

  • Kodi anamukhululukira chifukwa chiyani?

  • Kodi Yehova anasonyeza bwanji kuti anamukhululukira?

Mfumu Manase

Mtumwi Petulo

Kodi ineyo ndingatsanzire bwanji khalidwe la Yehova lokhululuka?