• Nyimbo Na. 21 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Kodi Yehova Akatikhululukira Machimo, Amawakumbukirabe?”: (10 min.)

  • Ezek. 18:19, 20​—Yehova amaimba mlandu munthu aliyense malinga ndi zochita zake (w12 7/1 18 ¶2)

  • Ezek. 18:21, 22​—Yehova ndi wokonzeka kukhululukira anthu amene alapa ndipo akatero samawaimbanso mlandu (w12 7/1 18 ¶3-7)

  • Ezek. 18:23, 32​—Yehova amawononga oipa pokhapokha ngati wawachenjeza koma sakufuna kusintha (w08 4/1 8 ¶4; w06 12/1 27 ¶11)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Ezek. 18:29​—N’chifukwa chiyani Aisiraeli anayamba kuganiza kuti Yehova akulakwitsa zinthu, nanga kodi ifeyo tingapewe bwanji mtima umenewu? (w13 8/15 11 ¶9)

  • Ezek. 20:49​—Kodi n’chifukwa chiyani anthu ankaganiza kuti Ezekieli ‘akunena miyambi,’ nanga ifeyo tikupezapo chenjezo lotani? (w07 7/1 14 ¶3)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 20:1-12

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) 1 Yoh. 5:19​—Kuphunzitsa Choonadi. Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Gen. 3:2-5​—Kuphunzitsa Choonadi. Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira. (Onani mwb16.08 8 ¶2.)

 • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w16.05 32​—Mutu: Kodi Tingasonyeze Bwanji Kusangalala Tikamva Chilengezo Choti Munthu Wina Wabwezeretsedwa?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU