ONANI

Buku la Ezekieli linaneneratu mwatsatanetsatane za mmene mzinda wa Turo udzawonongedwere.

  • 26:7-11

    Kodi ndani anawononga mzinda wa Turo patapita nthawi kuchokera mu 607 B.C.E.?

  • 26:4, 12

    Kodi ndani anatenga dothi ndi zogumuka za mabwinja a mzinda wa Turo M’chaka cha 332 B.C.E., n’kukazithira m’nyanja kuti apange njira pokawononga mbali ina ya mzindawo yomwe inali panyanja?

Kodi inuyo mukuyembekezera mwachidwi kudzaona kukwaniritsidwa kwa ulosi uti?