Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

July 31–August 6

EZEKIELI 24-27

July 31–August 6
 • Nyimbo Na. 81 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Ulosi Wonena za Kuwonongedwa kwa Turo Umatithandiza Kuti Tizikhulupirira Kwambiri Mawu a Yehova”: (10 min.)

  • Ezek. 26:3, 4​—Kutatsala zaka zoposa 250, Yehova ananeneratu kuti mzinda wa Turo udzawonongedwa (si 133 ¶4)

  • Ezek. 26:7-11​—Ezekieli anatchula mfumu komanso mtundu wa anthu womwe udzayambirire kuukira mzinda wa Turo (ce 216 ¶3)

  • Ezek. 26:4, 12​—Ezekieli ananeneratu kuti mpanda, fumbi komanso nyumba za mumzinda wa Turo zidzaponyedwa m’madzi (it-1 70)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Ezek. 24:6, 12​—Kodi dzimbiri la mphika likuimira chiyani? (w07 7/1 14 ¶2)

  • Ezek. 24:16, 17​—N’chifukwa chiyani Ezekieli sankafunika kusonyeza chisoni pamene mkazi wake anamwalira? (w88 9/15 21 ¶24)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 25:1-11

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Kapepala kalikonse​—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Kapepala kalikonse​—Mufotokozereni za vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (Koma musaonetse vidiyoyi).

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 23 ¶13-15​—Muitanireni kumisonkhano.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU