• Nyimbo Na. 52 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Kodi Muli ndi Mtima Wofewa Ngati Mnofu?”: (10 min.)

  • Ezek. 11:17, 18​—Yehova analonjeza kuti adzabwezeretsa kulambira koona (w07 7/1 11 ¶4)

  • Ezek. 11:19​—Yehova angatipatse mtima woti tizimvera malamulo ake (w16.05 15 ¶9)

  • Ezek. 11:20​—Yehova amafuna kuti tizigwiritsa ntchito zimene timaphunzira

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Ezek. 12:26-28​—Kodi mavesiwa akusonyeza kuti atumiki a Yehova ali ndi udindo wotani? (w07 7/1 13 ¶8)

  • Ezek. 14:13, 14​—Kodi tikuphunzira chiyani pa kutchulidwa kwa anthu atatu amene ali m’mavesiwa? (w16.05 26 ¶13; w07 7/1 13 ¶9)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 12:1-10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Kukambirana “Zitsanzo za Ulaliki.” Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 154

 • Zofunika Pampingo: (15 min.) Mukhoza kukambirana mfundo zimene tikuphunzira mu Buku Lapachaka. (yb17 41-43)

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 3 ¶1-12, komanso tsamba 30-31

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 43 ndi Pemphero