Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  July 2017

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 21-23

Ufumu Unaperekedwa kwa Amene Ndi Woyenerera Mwalamulo

Ufumu Unaperekedwa kwa Amene Ndi Woyenerera Mwalamulo
ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

Pokwaniritsa ulosi wa Ezekieli, Yesu ndi amene anali “woyenerera mwalamulo” kukhala mfumu.

  • Gen. 49:10

    Kodi Mesiya anabadwira mu mtundu uti?

  • 2 Sam. 7:12, 16

    Kodi ndi ufumu uti umene Yehova ananena kuti udzakhazikika mpaka kalekale

  • Mat. 1:16

    Kodi Mateyu anati Yesu anali wa mu mzera wobadwira chifukwa cha kholo liti?

Kodi tikuphunzirapo chiyani za Yehova pa zomwe anachita posankha Yesu kukhala mfumu yoikidwa mwalamulo?