Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

July 24-30

EZEKIELI 21-23

July 24-30
 • Nyimbo Na. 99 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Ufumu Unaperekedwa kwa Amene Ndi Woyenerera Mwalamulo”: (10 min.)

  • Ezek. 21:25​—“Mtsogoleri wa Isiraeli woipa” anali Mfumu Zedekiya (w07 7/1 13 ¶11)

  • Ezek. 21:26​—Anthu a m’banja la Davide omwe ankalamulira ali ku Yerusalemu anasiya kukhala mafumu (w11 8/15 9 ¶6)

  • Ezek. 21:27​—Yesu Khristu ndi amene ali “woyenerera mwalamulo” kukhala Mfumu (w14 10/15 10 ¶14)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Ezek. 21:3​—Kodi “lupanga” limene Yehova anasolola m’chimake ndi chiyani makamaka? (w07 7/1 14 ¶1)

  • Ezek. 23:49​—Kodi chaputala 23 chikusonyeza kuti Aisiraeli ndi Ayuda anachita tchimo lotani, nanga ifeyo tikuphunzirapo chiyani? (w07 7/1 14 ¶6)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 21:1-13

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 93

 • Tizisonyeza Ulemu Tikafika Pakhomo”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Ikambidwe ndi woyang’anira utumiki. Yambani ndi kuonetsa vidiyo yofotokoza zimene tingachite kuti tizisonyeza ulemu tikafika pakhomo la munthu.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 4 ¶7-15 komanso tsamba 4446

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero