• Nyimbo Na. 104 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Tamandani Yehova Wakumva Pemphero”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Sal. 63:3—N’chifukwa chiyani kukoma mtima kwa Yehova n’kwabwino kuposa moyo? (w06 6/1 11 ndime 9)

  • Sal. 68:18—Kodi ndani amene anali “mphatso za amuna”? (w06 6/1 10 ndime 5)

  • Kodi ndaphunzira chiyani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 63:1–64:10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Konzekerani Zitsanzo za Ulaliki za Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani kavidiyo kosonyeza zitsanzo za ulaliki kenako kambiranani mfundo zimene tikuphunzirapo. Limbikitsani omvera kuti alembe ulaliki umene angakonde kugwiritsa ntchito.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU