Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU–NDANDANDA YA MISONKHANO JULY 2016

July 18-24

MASALIMO 74-78

July 18-24
 • Nyimbo Na. 110 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Tizikumbukira Ntchito za Yehova”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Sal. 78:2—Kodi lembali linakwaniritsidwa bwanji kudzera mwa Mesiya? (w11 8/15 11 ndime 14)

  • Sal. 78:40, 41—Mogwirizana ndi mavesi amenewa, kodi zochita zathu zingakhudze bwanji Yehova? (w12 11/1 14 ndime 5; w11 7/1 10)

  • Kodi ndaphunzira chiyani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 78:1-21

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 15

 • Zofunika pampingo: (10 min.)

 • “Yehova . . . Analenga Zinthu Zonse”: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi yomwe imapezeka pa webusaiti ya jw.org/ny yakuti Yehova . . . Analenga Zinthu Zonse.” (Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA.) Mukamaliza, itanani ana angapo kuti abwere kutsogolo ndipo afunseni mafunso okhudza vidiyoyi.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 2 ndime 13-23

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero