CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Paulo Anapita ku Roma”: (10 min.)

  • Mac. 27:23, 24​—Mngelo anauza Paulo kuti iyeyo ndi onse omwe anali m’ngalawamo apulumuka mphepo yamkuntho (bt 208 ¶15)

  • Mac. 28:1, 2​—Ngalawa imene Paulo anakwera inasweka pachilumba cha Melita (bt 209 ¶18-210, ¶21)

  • Mac. 28:16, 17​—Paulo anakafika bwinobwino ku Roma (bt 213 ¶10)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Mac. 27:9​—Kodi “nthawi ya kusala kudya kwa Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo” imatanthauza chiyani? (“kusala kudya kwa Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mac. 27:9, nwtsty)

  • Mac. 28:11​—Kodi chochititsa chidwi n’chiyani ndi kutchulidwa kwa chizindikiro chomwe chinali pangalawa yomwe Paulo anakwera? (“Ana . . . a Zeu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mac. 28:11, nwtsty)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mac. 27:1-12 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU