●○○ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi inuyo mumaona kuti Baibulo ndi lothandizabe masiku ano?

Lemba: 2 Tim. 3:16

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi m’Baibulo muli uthenga wotani?

○●○ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA

Funso: Kodi m’Baibulo muli uthenga wotani?

Lemba: Mat. 6:10

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Ufumu wa Mulungu udzachita chiyani?

○○●ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI

Funso: Kodi Ufumu wa Mulungu udzachita chiyani?

Lemba: Dan. 2:44

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi zimenezi zidzakhudza bwanji anthu omwe ali padzikoli?