Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  January 2017

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 43-46

Yehova Ndi Mulungu Yemwe Amalosera Zoona

Yehova Ndi Mulungu Yemwe Amalosera Zoona
ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

Kutatsala zaka pafupifupi 200 kuti mzinda wa Babulo uwonongedwe, Yehova ananeneratu mwatsatanetsatane kudzera mwa Yesaya zimene zidzachitike pogonjetsa mzindawo.

44:27–45:2

  • Koresi ndi amene adzagonjetse Babulo

  • Zitseko za mzindawo zidzakhala zotsegula

  • Mtsinje wa Firate, womwe unkateteza mzindawu, ‘udzaumitsidwa’