Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  January 2017

January 16-22

YESAYA 34-37

January 16-22
 • Nyimbo Na. 31 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Hezekiya Anadalitsidwa Chifukwa cha Chikhulupiriro Chake”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yes. 35:8—Kodi “Msewu wa Chiyero” unali chiyani, nanga ndi ndani amene ankayenera kuyendamo? (w08 5/15 26 ¶4; 27 ¶1)

  • Yes. 36:2, 3, 22—Kodi Sebina anasonyeza bwanji chitsanzo chabwino atachotsedwa pa udindo? (w07 1/15 9 ¶1)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 36:1-12

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Mat. 24:3, 7, 14—Kuphunzitsa Choonadi—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) 2 Tim. 3:1-5—Kuphunzitsa Choonadi—Musiyireni khadi lodziwitsa anthu za JW.ORG.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 33 ¶11-12—Muitanireni kumisonkhano.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 91

 • Inu Yehova, . . . Chikhulupiriro Changa Chili mwa Inu: (15 min.) Mafunso ndi mayankho. Yambani ndi kuonetsa vidiyo yakuti “Inu Yehova, . . . Chikhulupiriro Changa Chili mwa Inu”—Kachigawo Kochepa.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 15 ¶15-26 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 134

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 96 ndi Pemphero