Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu–Ndandanda ya Misonkhano  |  January 2016

January 25-31

EZARA 6-10

January 25-31
 • Nyimbo Na. 10 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yehova Amafuna Kuti Tizimutumikira ndi Mtima Wonse”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Ezara 9:1, 2—N’chifukwa chiyani kukwatirana ndi anthu a mitundu ina kunali koopsa? (w06 1/15 20 ndime 1)

  • Ezara 10:3—N’chifukwa chiyani ana anachotsedwa pamodzi ndi akazi? (w06 1/15 20 ndime 2)

  • Kodi ndaphunzira chiyani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: Ezara 7:18-28 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gawirani kabuku kakuti Uthenga Wabwino, kenako kambiranani phunziro 8, funso 1 ndime 1. Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Chitani chitsanzo chosonyeza ulendo wobwereza kwa munthu amene analandira kabuku kakuti Uthenga Wabwino. Mukambirane naye phunziro 8, funso 1 ndime 2. Mumuuze nkhani imene mudzaphunzire ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) Chitani chitsanzo cha munthu akuchititsa phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Uthenga Wabwino phunziro 8, funso 2.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU