ONANI

MANASE

Yehova analola kuti amangidwe ndi Asuri n’kupita ku Babulo

MU ULAMULIRO WAKE ASANAMANGIDWE

 • Anamanga maguwa ansembe a milungu yonyenga

 • Anapereka nsembe ana ake

 • Anapha anthu osalakwa

 • Analimbikitsa zamizimu m’dziko lonse

MU ULAMULIRO WAKE ATAMASULIDWA

 • Anadzichepetsa kwambiri

 • Anapemphera kwa Yehova n’kupereka nsembe

 • Anawononga maguwa ansembe a milungu yonyenga

 • Analimbikitsa Aisiraeli onse kuti azitumikira Yehova

YOSIYA

MU ULAMULIRO WAKE

 • Anafunafuna Yehova

 • Anayeretsa Yuda ndi Yerusalemu

 • Anakonza nyumba ya Yehova ndipo anapeza buku la Chilamulo