Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  January 2016

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 2 MBIRI 29-32

Tizichita Khama Polambira Yehova

Tizichita Khama Polambira Yehova
ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

Hezekiya anathandiza anthu kuti ayambenso kulambira Yehova

29:10-17

 • 746-716 B.C.E.

  Hezekiya Analamulira Kuyambira mu

 • NISANI 746 B.C.E.

  • Tsiku loyamba mpaka la 8: Anayeretsa Bwalo la Mkati

  • Tsiku la 9 mpaka la 16: Anayeretsa Nyumba ya Yehova

  • Anapereka nsembe yophimba machimo a Aisiraeli onse ndipo anthu anayambanso kulambira Mulungu

 • 740 B.C.E.

  Mzinda wa Samariya Unawonongedwa

Hezekiya anasonkhanitsa anthu kuti alambire Yehova

30:5, 6, 10-12

 • Anthu anatumidwa kukapereka makalata olengeza za Pasika. Anapereka makalatawa kuyambira ku Beere-seba mpaka ku Dani

 • Ena ananyozera uthengawo koma ena anamvera