• Nyimbo Na. 114 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kukonzekera Zitsanzo za Ulaliki za Mwezi Uno. (15 min.) Nkhani yokambirana. Chitani chitsanzo chosonyeza zimene tingachite pogawira magazini a Nsanja ya Olonda kenako kambiranani mfundo zimene mwaphunzirapo. Fotokozani zimene wofalitsa wachita kuti adzapange ulendo wobwereza. Chitani chimodzimodzi ndi chitsanzo chachiwiri chogawira Nsanja ya Olonda komanso kabuku ka Uthenga Wabwino. Onaninso mfundo zina pa mutu wakuti, “Kuphunzitsa Anthu Pogwiritsa Ntchito Kabuku ka Uthenga Wabwino.” Limbikitsani omvera kuti alembe zitsanzo za ulaliki zimene angakonde kugwiritsa ntchito pamalo amene apatsidwa.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 127

  • Tizigwira Nawo Ntchito Yomanga Komanso Kukonza Malo Olambirira.” (15 min.) Nkhani yokambirana. Funsani abale ndi alongo amene anagwirako ntchito yomanga Nyumba ya Ufumu kuti afotokoze zosangalatsa zimene anakumana nazo. Kenako funsani m’bale amene amayang’anira ntchito yoyeretsa komanso kukonza Nyumba ya Ufumu, kuti afotokoze mwachidule zimene mpingo unakonza zokhudza kusamalira nyumbayo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 24 ndime 1-10 (30 min.)

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu wa Mawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 142 ndi Pemphero

    Kumbukirani kuti, muyenera kuika nyimboyi kuti onse aimvetsere kenako muibwerezenso kuti onse aimbe nawo