Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Alongo akugwiritsa ntchito kabuku kakuti Uthenga Wabwino ku Madagascar

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU January 2016

Zitsanzo za Ulaliki

Zitsanzo za ulaliki wa magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! komanso kabuku ka Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu. Potengera zitsanzozi, konzani njira imene mungagwiritse ntchito.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tizichita Khama Polambira Yehova

Yerekezerani kuti mukuona Hezekiya akuchita khama. Gwiritsani ntchito zithunzi, mapu ndiponso tchati chofotokoza zimene zinachitika pa 2 Mbiri 29-30 kuti zikuthandizeni

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

Kuphunzitsa Anthu Pogwiritsa Ntchito Kabuku ka Uthenga Wabwino

Mfundo 5 zimene mungatsatire mukamaphunzitsa anthu pogwiritsa ntchito kabuku ka Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu

MOYO WACHIKHRISTU

Tizigwira Nawo Ntchito Yomanga Komanso Kukonza Malo Olambirira

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timakonda kutumikira pamalo athu olambirira?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amakhululukira Munthu Amene Walapa Kuchokera Pansi pa Mtima

Yehova anaona kuti Manase analapa kuchokera pansi pa mtima. Kodi zimene anachita asanamangidwe zikusiyana bwanji ndi zimene anachita atamasulidwa ku Babulo. (2 Mbiri 33-36)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amakwaniritsa Malonjezo Ake

Tchati chosonyeza zimene zinachitika pa Ezara 1-5. Ayuda amene anabwerera anayamba kulambira Yehova ndipo anamanganso kachisi ngakhale kuti panali mavuto ambiri.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amafuna Kuti Tizimutumikira ndi Mtima Wonse

Ezara ndi anthu amene anabwerera nawo ku Yerusalemu anafunika kukhala ndi chikhulupiriro cholimba, kukonda Yehova komanso kulimba mtima. Onani mmene anayendera pamapu ndi tchatichi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kuwonjezera Luso Lathu Mu Utumiki—Muzisiya Mafunso Oti Mudzakambirane Ulendo Wotsatira

Mfundo zitatu zimene muyenera kutsatira mukabwerera kwa munthu amene anasonyeza chidwi.