8:19-21

  • “Chilengedwe”: anthu amene akuyembekezera kudzakhala padziko lapansi

  • ‘Ulemelero wa ana a Mulungu udzaonekera’: pamene odzozedwa adzathandiza Yesu kuwononga dziko loipa la Satanali

  • “Maziko a chiyembekezo”: zimene Yehova akulonjeza kuti adzatipulumutsa kudzera mu imfa komanso kuukitsidwa kwa Yesu

  • ‘Kumasulidwa ku ukapolo wa kuvunda’: anthu adzayamba kumasulidwa pang’onopang’ono kuchokera ku mavuto amene amabwera chifukwa cha uchimo ndi imfa