16:21-23

  • N’kutheka kuti Petulo anauza Yesu kuti adzikomere mtima ndi cholinga chabwino koma mwansanga Yesu anawongolera maganizo olakwika amene Petulo anali nawo

  • Yesu ankadziwa kuti imeneyo sinali nthawi yoti ‘adzikomere mtima.’ Akanachita zimenezi akanakhala akuchita zimene Satana ankafuna

16:24

Yesu anatchula zinthu zitatu zotsatirazi zomwe tiyenera kuchita ngati tikufuna kuti Mulungu azititsogolera. Kodi zinthu zimenezi zikutanthauza chiyani?

  • Kudzikana:

  • Kunyamula mtengo wozunzikirapo:

  • Kutsatira Yesu mosalekeza: