CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Kodi Mumayendera Maganizo a Ndani?”: (10 min.)

  • Mat. 16:21, 22​—Petulo analola kuti kutengeka maganizo kuzilamulira kaganizidwe kake (w07 2/15 16 ¶17)

  • Mat. 16:23​—Petulo anasiya kuyendera maganizo a Mulungu (w15 5/15 13 ¶16-17)

  • Mat. 16:24​—Akhristu ayenera kumayendera maganizo a Mulungu (w06 4/1 23 ¶9)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Mat. 16:18​—Kodi ndi ndani amene anali thanthwe lomwe Yesu anamangapo mpingo wachikhristu? (“Iwe ndiwe Petulo, ndipo pathanthwe ili” “mpingomfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 16:18, nwtsty)

  • Mat. 16:19​—Kodi “makiyi a Ufumu wakumwamba” amene Yesu anapatsa Petulo anali chiyani? (“makiyi a Ufumu wakumwamba” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 16:19, nwtsty)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 16:1-20

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri.

 • Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

 • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU