CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yesu Amadyetsa Anthu Ambiri Kudzera Mwa Anthu Ochepa”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Mat. 15:7-9​—N’chifukwa chiyani tiyenera kupewa chinyengo? (Onyenga” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 15:7, nwtsty)

  • Mat. 15:26​—Kodi n’kutheka kuti Yesu ankatanthauza chiyani pamene ananena mawu akuti “tiagalu”? (ana . . . tiagalu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 15:26, nwtsty)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 15:1-20

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

 • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

 • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w15 9/15 16-17 ¶14-17​—Mutu: Tizitsatira Yesu Kuti Tilimbitse Chikhulupiriro Chathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU