CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Khristu Anavutika Chifukwa cha Ife”: (10 min.)

  • Yes. 53:3-5—Ananyozedwa ndiponso kuphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu (w09 1/15 26 ¶3-5)

  • Yes. 53:7, 8—Anapereka yekha moyo wake kuti atipulumutse (w09 1/15 27 ¶10)

  • Yes. 53:11, 12—Popeza kuti Yesu anakhala wokhulupirika mpaka imfa, tili ndi mwayi woti Mulungu akhoza kutiona kuti ndife olungama (w09 1/15 28 ¶13)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yes. 54:1—Kodi “mkazi wosabereka” amene akutchulidwa mu ulosiwu ndi ndani, nanga “ana” ake ndi ndani? (w06 3/15 11 ¶2)

  • Yes. 57:15—Kodi Yehova “amakhala” bwanji ndi anthu “opsinjika” ndiponso “onyozeka”? (w05 10/15 26 ¶3)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 57:1-11

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) bm—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) bm 30-31—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 13-14 ¶16-17—Ngati n’zotheka, chitsanzochi chikhale cha bambo akuphunzira ndi mwana wake.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU