Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

February 20-26

YESAYA 58-62

February 20-26

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Tikalengeze za Chaka cha Yehova Chokomera Anthu Mtima”: (10 min.)

  • Yes. 61:1, 2—Yesu anadzozedwa kuti ‘alengeze chaka cha Yehova chokomera anthu mtima’ (ip-2 322 ¶4)

  • Yes. 61:3, 4—Yehova amatipatsa “mitengo ikuluikulu ya chilungamo” kuti izitithandiza pa ntchito yake (ip-2 326-327 ¶13-15)

  • Yes. 61:5, 6—“Anthu ochokera kwina” amagwirizana ndi “ansembe a Yehova” pogwira ntchito yaikulu yolalikira padziko lonse (w12 12/15 25 ¶5-6)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yes. 60:17—Kodi Yehova wakwaniritsa bwanji lonjezoli m’masiku otsiriza ano? (w15 7/15 9-10 ¶14-17)

  • Yes. 61:8, 9—Kodi “pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale” n’chiyani, nanga “ana” ndi ndani? (w07 1/15 11 ¶6)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 62:1-12

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.1 chikuto

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.1 chikuto

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 15 ¶19—Ngati n’zotheka, chitsanzochi chikhale cha mayi akuphunzira ndi mwana wake wamkazi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU