Mtsikana wa Mboni akufotokozera anzake a m’kalasi zimene walemba zokhudza chilengedwe

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU February 2017

Zitsanzo za Ulaliki

Zitsanzo za ulaliki wa Galamukani! ndiponso zomwe tingachite pophunzitsa anthu zinthu zabwino zimene Mulungu akufuna kuchita posachedwapa padzikoli. Gwiritsani ntchito zitsanzozi kuti mupange ulaliki wanuwanu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kumvera Yehova Kumabweretsa Madalitso

Yehova Mulunga amatisonyeza mwachikondi zimene tiyenera kuchita pamoyo wathu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Khristu Anavutika Chifukwa cha Ife

Imfa ya Yesu inathandiza kutsutsa zimene Satana ananena zoti atumiki a Mulungu sangakhale okhulupirika atakumana ndi mavuto.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzithandiza Ana Anu Kuti Azikhulupirira Kwambiri Mlengi

Kodi ana anu amakhulupirira kuti moyo unayamba bwanji? Kodi mungawathandize bwanji kuti ayambe kukhulupirira kuti Yehova Mulungu ndi amene analenga zonse?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

‘Tikalengeze za Chaka cha Yehova Chokomera Anthu Mtima’

Kodi chaka cha Yehova chokomera anthu mtima ndi chaka chenicheni? Kodi nthawi imeneyi ikugwirizana bwanji ndi ntchito yolalikira za Ufumu?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Tizigwiritsa Ntchito Mwanzeru Mabuku Ndiponso Magazini

Pamafunika ndalama zambiri komanso pamakhala ntchito yaikulu kuti mabukuwa asindikizidwe ndiponso kutumizidwa kumipingo padziko lonse. Tizichita zinthu mozindikira tikamagawira mabuku ndi magazini

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tidzasangalala Kwambiri ndi Kumwamba Kwatsopano Komanso Dziko Lapansi Latsopano

Kodi lonjezo la Mulungu la “kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano” likutikhudza bwanji?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Tizisangalala ndi Chiyembekezo Chathu

Chiyembekezo chili ngati nangula amene amathandiza kuti sitima isasunthe. Zili choncho chifukwa chimatithandiza kuti tisasokonezeke mwauzimu tikakumana ndi mavuto aakulu okhala ngati mafunde oopsa.