Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu–Ndandanda ya Misonkhano  |  February 2016

February 29–March 6

ESITERE 1-5

February 29–March 6
 • Nyimbo Na. 86 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Perekani kabuku kakuti Mverani Mulungu. Muuzeni zimene mudzakambirane mukadzabweranso.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Chitani chitsanzo chosonyeza kuti mwakumananso ndi munthu amene analandira kabuku kakuti Mverani Mulungu ndipo kambiranani tsamba 2 ndi 3. Muuzeni nkhani imene mudzaphunzire pa ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) Chitani chitsanzo chosonyeza mukuphunzira ndi munthu yemwe analandira kabuku kakuti Mverani Mulungu. Gwiritsani ntchito tsamba 4 ndi 5 la kabuku kakuti Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha. (km 7/12 2-3 ndime 4)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 71

 • Zofunika pampingo: (10 min.)

 • Fotokozani Mmene Ndandanda Yatsopano ya Misonkhano Yakuthandizirani?: (5 min.) Nkhani yokambirana. Funsani omvera kuti afotokoze mmene ndandanda yatsopanoyi yawathandizira. Alimbikitseni kuti azikonzekera bwino misonkhanoyi kuti azipindula kwambiri.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 26 ndime 18-23, ndi bokosi tsa. 269 (30 min.)

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu wa Mawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 149 ndi Pemphero