Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | NEHEMIYA 5-8

Nehemiya Anali Woyang’anira Wabwino

Nehemiya Anali Woyang’anira Wabwino

Tishiri 455 B.C.E.

8:1-18

  1. N’kutheka kuti panthawiyi m’pamene Nehemiya anasonkhanitsa anthu kuti alambire Yehova

  2. Anthu anasangalala kwambiri

  3. Anthu amene anali mitu ya mabanja anasonkhana kuti aone zimene angachite kuti azitsatira kwambiri Chilamulo cha Mulungu

  4. Anthu anakonzekera kuchita Chikondwerero cha Misasa