Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  February 2016

February 8-14

NEHEMIYA 5-8

February 8-14
 • Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Nehemiya Anali Woyang’anira Wabwino”: (10 min.)

  • Neh. 5:1-7—Nehemiya ankamvetsera zimene anthu ankanena n’kuchitapo kanthu (w06 2/1 9 ndime 2)

  • Neh. 5:14-19—Nehemiya anali wodzichepetsa, wanzeru komanso sankadzikonda (w06 2/1 10 ndime 4)

  • Neh. 8:8-12—Nehemiya ankaphunzitsa anthu Mawu a Mulungu (w06 2/1 11 ndime 4)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Neh. 6:5—N’chifukwa chiyani Sanibalati anatumiza “kalata yosatseka” kwa Nehemiya? (w06 2/1 9 ndime 3)

  • Neh. 6:10-13—N’chifukwa chiyani Nehemiya sanamvere zimene Semaya anamuuza? (w07 7/1 30 ndime 15)

  • Kodi ndaphunzira chiyani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: Neh. 6:14-19; 7:1-7a (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) M’patseni Galamukani! yatsopano pogwiritsa ntchito mutu wapachikuto. Muuzeni zimene mudzakambirane mukadzabweranso.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Chitani chitsanzo chosonyeza ulendo wobwereza kwa munthu amene anasangalala mutamupatsa Galamukani! yatsopano pogwiritsa ntchito mutu wapachikuto. Muuzeni nkhani yomwe mudzaphunzire mukadzabweranso.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) Chitani chitsanzo chosonyeza mukuphunzira Baibulo ndi munthu. (bh 28-29 ndime 4-5)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 62

 • Kodi ‘Mukuyesetsa Kuti Mukhale Woyang’anira’?: (15 min.) Nkhani yokambidwa ndi mkulu yochokera mu Nsanja ya Olonda ya September 15, 2014, tsamba 3-6. Onetsani vidiyo yakuti Abale Yesetsani Kuti Mukhale Oyang’anira! yomwe inatuluka pa JW Broadcasting mu December 2015. Tsindikani zifukwa zoyenera zotilimbikitsa kuti tiyesetse kukhala oyang’anira komanso mmene tingachitire zimenezi. Limbikitsani abale kuti ayesetse kuti akhale atumiki othandiza kapena akulu.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 25 ndime 17-21, bokosi tsa. 259 (30 min.)

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 125 ndi Pemphero