Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  February 2016

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | NEHEMIYA 12-13

Zimene Tikuphunzira kwa Nehemiya

Zimene Tikuphunzira kwa Nehemiya

Nehemiya anali wakhama poteteza kulambira koona

13:4-9, 15-21, 23-27

  • Mkulu wa ansembe dzina lake Eliyasibu analola kuyendera maganizo a Tobiya, yemwe sankalambira Yehova

  • Eliyasibu anakonzera Tobiya chipinda m’bwalo la nyumba ya Mulungu

  • Nehemiya anataya kunja katundu wa Tobiya n’kuyeretsa chipindacho kuti chizigwira ntchito yake yoyenera

  • Nehemiya anapitiriza kuyeretsa Yerusalemu